Bushiri wakanitsitsa za ndale: “ Chonde sindikuyambisa chipani, sindikupisana nawo, siyani kufalisa izi.”

M’neneri Shepherd Bushiri wati alibe malingaliro ofuna kuyamba ndale kapena kupikisana nawo pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko chaka cha mawa. A Bushiri, omwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa ECG-The Jesus Nation ati iwo ndi mtumiki wa Mulungu amene cholinga chawo chakhazikika pogwira ntchito ndi boma lolamula ndipo adzapitiriza kutero. Yemwe amawayankhulira, Aubrey Kusakala wati […]

The post Bushiri wakanitsitsa za ndale: “ Chonde sindikuyambisa chipani, sindikupisana nawo, siyani kufalisa izi.” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください