Shepherd Bushiri wapereka thandizo la chakudya kwa anthu omwe akhala akukhudziwa ndi njala kwa mfumu yaikulu Mbenje m’boma la Nsanje. Izi zinatsatira maripoti oti anthu ku delari akhala akudya zakudya monga nyika komanso zikhawo pofuna kupewa imfa ndi njala. Mchitidwe wu, unapangitanso kuti anthu ena akumane ndi ngozi zina kuphatikizapo kulumidwa ndi n’gona. Ndipo polankhula […]
The post Bushiri apitiliza ntchito yogawa chakudya: Pano wafika ku Nsanje appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.