Bus ya pa Mzuzu University yomwe nambala yake ndi MZ10315 yachita ngozi pa Kanduli m’mawa uno pamene ophunzira a sukulu ya ukachenjedeyi anali pa ulendo opita m’boma la Nkhata-Bay. M’modzi mwa ophunzira amene anali nawo pa ulendowu anauza Malawi24 kuti zikuonetsa kuti ngoziyi yachitika kamba kakuti Bus yo inaduka mabuleki. Pakadali pano omwe avulala athamangira […]
The post Bus ya Mzuni yachita ngozi lero appeared first on Malawi 24.