Bungwe la United Nations liyamikila Chakwera kamba kopititsa patsogolo ntchito zotukula amai mdziko muno

Bungwe la United Nations (UN) layamikila mtsogogoleri wadziko lino a Dr Lazarus McCarthy Chakwera kamba koonetsa chidwi pa ntchito yotukula amai mdziko muno. Rebecca Adda-Dontoh walankhula izi dzulo pame mtsogoleri wadziko lino anakumana anthu ogwira ntchito kumabungwe a UN. M’mawu awo a Dontoh anayamikila a Chakwera kuti amai akusimba lokoma mdziko muno chifukwa chakwera akuwapatsa […]

The post Bungwe la United Nations liyamikila Chakwera kamba kopititsa patsogolo ntchito zotukula amai mdziko muno appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください