Oyankhulapo pa nkhani zochitika mdziko muno adzudzula bungwe la Mulhako wa Alhomwe chifukwa chosaitana mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ku mwambo omwe ukuyembekezera kuchitika pa 9 October, 2022 kwa Chonde ku Mulanje. A Latina Matenje adzudzula zomwe zachitikazi chifukwa iwo akuona kuti zachitika pa zifukwa za ndale. A Matenje atsutsa zomwe akunena a […]
The post Bungwe la Mulhako ladzudzulidwa posaitana a Chakwera ku mwambo wa chikhalidwe appeared first on Malawi 24.