Bungwe loona za ufulu wa anthu mdziko muno la Malawi Human Rights Resource Centre (MHRRC) lati dziko la Malawi likuyenera kusintha mwa zina zomwe zimalepheletsa atsikana ndi amayi kupeza nawo thandizo lochotsa pakati motetezedwa. A Enock Chinkhuntha omwe ndi mkulu wa MHRRC polojekiti ndi omwe anena izi kumaphunziro atolankhani nkhani omwe anachitika dzulo la chisanu […]
The post Bungwe la MHRRC lati dziko lino likuyenera kusintha zinthu zina pankhani yokhudza kuchotsa pakati motetezedwa appeared first on Malawi 24.