Bungwe la MEC lati kugwiritsa ntchito zipangizo za boma pa misonkhano ya ndale ndikosaloledwa

Bungwe lowona za chisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lati kugwiritsa ntchito zipangizo za boma monga galimoto pamisonkhano ya ndale yokopa anthu pachisankho ndikosaloledwa ndipo bungweli lati aliyense opezeka akuchita izi adzayimbidwa mlandu. M’modzi mwa makomishonala a MEC a Richard Chapweteka ndi womwe ayankhula izi mu mzinda wa Zomba pomwe amafotokozera atolankhani za […]

The post Bungwe la MEC lati kugwiritsa ntchito zipangizo za boma pa misonkhano ya ndale ndikosaloledwa appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください