Bungwe la Malawi Kickboxing Association lati likufuna ndalama zocholuka zoyendetsera masewero otibulana a kickboxing ndipo lapempha Boma kudzera ku Malawi Sports Council kuti liwathandidze. Mlembi wamkulu ku Bungwe la Malawi Kickboxing Association a Bright Limani ndiwomwe ayankhula izi Lolemba ku China Complex ku Zomba komwe kudali masewero a Inter Club Kickboxing Championship ofuna kusankha akaswiri […]
The post Bungwe la Malawi Kickboxing Association lati likufuna ndalama zocholuka zoyendetsera masewero appeared first on Malawi 24.