Buluzi wa ize adapanidwa mchitseko: Ena ku Luanar yauma kamba ndi nyani m’mayeso

Sukulu ya ukachenjede ya Luanar yapereka zilango kwa ophunzira okwana 19 kamba kopezeka olakwa pa mlandu owonera mayeso ndipo atatu mwa ophunzirawa awachotsa sukulu. Ophunzira pamene khumi ndi anayi ayimitsidwa sukulu kwa zaka ziwili, ena chaka chimodzi pamene awili alandira chenjezo. Malingana ndi kalata yomwe sukuluyi yatulutsa, ophunzirawa alandira zilangozi kamba kopezeka ndi lamya za […]

The post Buluzi wa ize adapanidwa mchitseko: Ena ku Luanar yauma kamba ndi nyani m’mayeso appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください