BULU WATING’AMBA MNTHITI: Castel yakweza mtengo wa mowa

Bulu wating’amba mnthiti, wating’ambiranso zovala, Kampani ya Castel Malawi yakweza mtengo wa chakumwa chake chaukali chosiyanasiyana potsatira kutsika mphamvu kwa ndalama ya Kwacha.

Malinga ndi kalata yomwe kampaniyi yatulutsa yomwe wasayinira ndi mkulu wa zamalonda Johan Maree mitengo yatsopanoyi iyamba kugwira ntchito lero lachisanu pa 10 November.

Iwo afotokozanso kuti chakumwa chija cha Malawi Gin,Premier Brandy komanso Vodka mtengo wake sunasinthe ngakhale ndalama ya dziko linoyi yachepa mphamvu.

The post BULU WATING’AMBA MNTHITI: Castel yakweza mtengo wa mowa appeared first on Malawi Voice.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください