Bwalo la Principal Resident Magistrate ku Zomba lapereka belo kwa mkulu wa Bungwe la Malawi First a Bon Kalindo koma apolisi amanganso a Kalindo atangotuluka mu bwalo la milandu pankhani yokhudza zipolowe za ku Mangochi pa nthawi yomwe adachititsa mademo. Bwaloli linakana pempho lomwe adapempha woyimira Boma pamilandu loti a Kalindo asawapatse belo kuwopa kuti […]
The post Bon Kalindo wamangidwanso bwalo ku Zomba litamupatsa belo appeared first on Malawi 24.