M’modzi mwa anthu omwe amayankhulapo za ulamuliro wabwino komanso amamenyera ufulu wa anthu mdziko muno Bon Kalindo wati zomwe akukambirana aphungu akunyumba ya malamulo kuti phungu akachoka pampando ngati anthu amdera lake sadamusankhenso adzilandira malipiro mwezi uliwonse mpaka moyo wake onse ndi zinthu zopanda pake ndipo wati izi zipangitsa kuti chuma cha dziko lino chipitilire […]
The post Bon Kalindo sakugwirizana ndi zoti aphungu azilandira ndalama moyo wao onse appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 
