Nduna ya za chuma, a Simplex Chithyola Banda yalonjeza kuti undunawu uwonjezera thumba la ndalama zopita ku ngongole za ulimi kudzera ku bungwe la NEEF kuti alimi ambiri apindule. A Chithyola ati ndi okhutira ndi momwe bungweli lagawira ngongoleyi nyengo ino komanso kuti anthu akubweza bwino. Iwo alankhula izi poyamba pa ulendo oyendera alimi omwe […]
The post Boma liwonjezera ndalama ku NEEF kuti alimi ambiri azitenga ngongole appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.