Boma lisamutsa msasa wa Dzaleka kuchoka ku Dowa kupita ku Chitipa

Boma lati lili ndi ganizo losamutsa msasa wa anthu othawa kwawo kuchoka ku Dowa kuti ukakhale m’boma la Chitipa. Izi lichita pofuna kuchepetsa kudzadzana kwa nzika za maiko enazi ku msasaku komanso pofuna kutsatira malamulo a dziko lonse lapansi oti msasa uzikhala makilomita 50 kuchokera pa chipata chadziko ndi dziko lina. Nthambi yowona umoyo wa […]

The post Boma lisamutsa msasa wa Dzaleka kuchoka ku Dowa kupita ku Chitipa appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください