Pomwe bwalo ya Kamuzu ili chikalambire ku Blantyre, dera lomwe linatchuka kwambiri nthawi ya ziwonetsero m’chaka cha 2019, Nsundwe, lalandira mphoto ya bwalo lochitilapo masewero lomwe boma lalengeza kuti likufuna kumanga kudelali. Nkhaniyi yadziwika pomwe khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yatulutsa chikalata chomemeza ma kampani omanga kuti yomwe ingachite mphumi igwire ntchito. Chikalatachi chikusonyeza kuti […]
The post Boma likufuna limange bwalo la masewero kwa Nsundwe appeared first on Malawi 24.