Boma likufuna kuti athu 50 pa 100 aliwonse azakhale ndi magetsi pofika 2030

Unduna woona mphamvu za magetsi m’dziko muno wati boma likufuna kuti pofika chaka cha 2030, anthu 50 pa anthu 100 aliwonse adzakhale akugwiritsa ntchito magetsi. Pakali pano anthu 27 pa anthu 100 aliwonse ndi amene akugwiritsa ntchito magetsi m’dziko muno. Mlembi wamkulu mu undunawu Alfonso Chikuni ndiye watsimikiza izi ndipo wati lingaliloli lidzatheka chifukwa unduna […]

The post Boma likufuna kuti athu 50 pa 100 aliwonse azakhale ndi magetsi pofika 2030 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください