Pamene ntchito younikanso ndondomeko ya maphunziro ili mkati, unduna wa za Maphunziro wati wayamba kumva maganizo a anthu pa zimene angafune kuti ziganiziridwe mu ndondomeko ya maphunziro ya tsopano. Undunawu ukuchita kauniuniyu mogwirizana ndi bungwe laboma la Malawi Institute of Education (MIE). Malingana ndi kalata yomwe undunawu walemba, kauniuni ameneyu ndiwokhudza maphunziro a m’sukulu za […]
The post Boma layamba kumva maganizo a anthu pa ndondomeko ya maphunziro appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.