Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ati a pulezidenti Lazarus Chakwera akanika kuyendetsa boma ndipo pali tsogolo lakuti chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) chibwerera mu boma. A Mutharika amayankhula izi dzulo ku msonkhano omwe anachititsa ku St Augustine 3 Primary School Ground mu boma la Mangochi. Malingana ndi a Mutharika, zinthu mdziko […]
The post Boma lawakanika: Mitengo yakwera ndi Chakwera – Mutharika asambwadza Tonse appeared first on Malawi24.