Boma lavomereza kuti likusowa makobiri olipilira mafumu

Pa galaundi pateleleratu pamene boma lavomereza kuti lilibe makobiri okwanira kuti lilipire mafumu ena mu dziko muno. Polankhula munyumba ya malamulo lachiwiri lapitali, nduna yoyang’anira za maboma ang’onoan’gono Blessings Chinsinga adauza nyumbayi kuti vuto li ladza kamba kosowa ndalama. Nduna yi idanena izi pame imayankha funso kuchokera kwa Phungu wa Zomba Ntonya, Ned Phoya. Phungu […]

The post Boma lavomereza kuti likusowa makobiri olipilira mafumu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください