Nduna ya zamasewero Uchizi Mkandawire yapempha apolisi kuti afufuze anthu omwe awononga mipando yoposa 200 ku bwalo la zamasewero la Bingu ku Lilongwe A Mkandawire ayankhula izi atayendera bwalo la zamasewero la Bingu komwe anthu anazula mipando 239 pomwe anakaonela mpira wa pakati pa Silver Strikers ndi Mighty Wanderers. Iwo anati apolisi agwire ntchito yawo […]
The post Boma lauza apolisi kuti amange anthu omwe anazula mipando ku Bingu appeared first on Malawi 24.