Boma latsindika ku mtundu wa a Malawi kuti limanga mabwalo amasewero a matimu a Mighty Mukuru Wanderers komanso FCB Nyasa Big Bullets mu mzinda wa Blantyre. Nduna yoona za achinyamata ndi masewero mdziko muno a Uchizi Mkandawire ndi omwe atsindika za nkhaniyi. Ntchito yomanga mabwalo amasewerawa alengezedwa koyamba mchaka cha 2020 koma idayamba yayima kaye. […]
The post Boma latsindika kuti limanga mabwalo amasewera a Bullets ndi Wanderers appeared first on Malawi 24.