Boma latsimikiza za chitetezo chokhazikika kwa achinyamata omwe akugwila ntchito dziko la Israel

Nduna ya zofalitsa nkhani yemwenso ndi m’neneri wa boma a Moses Kunkuyu wati kutsegula ofesi ya ukazembe m’dziko la Israel kuthandiza kuthana ndi mavuto omwe achinyamata akhathe kukumana nawo pomwe akugwila ntchito m’dzikoli. A Kunkuyu ayakhula izi pa msokhano wa olemba nkhani ku Lilongwe pomwe mwa zina amatambasula za ulendo wawo wa ku Israel pamodzi […]

The post Boma latsimikiza za chitetezo chokhazikika kwa achinyamata omwe akugwila ntchito dziko la Israel appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください