Boma lati mabwalo a Bullets ndi Wanderers amangidwa

Boma lati ndalama zokwana K800 miliyoni ziperekedwa ku ntchito yomangira mabwalo amasewero a FCB Nyasa Bullets ndi Mighty Mukuru Wanderers. Nduna ya zamasewero Uchizi Mkandawire ndi yomwe yanena izi lero. Malingana ndi a Mkandawire, ntchitoyi inaima m’mbuyomu kamba ka ngongole zina zomwe makontilakitara a mabwalowa anali nazo komanso kukwera mitengo kwa zipangizo zina zogwilira ntchitoyi. […]

The post Boma lati mabwalo a Bullets ndi Wanderers amangidwa appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください