Boma la mgwirizano wa Tonse lati likubweza ngongole ya US$800 miliyoni yomwe linatenga boma la chipani cha DPP ndipo izi zikuchititsa kuti ndalama zakunja zizisowa m’dziko muno. Wanena izi ndi nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu omwe amayankhula lero pa msonkhano wa olemba nkhani ku Lilongwe. Msonkhanowu unapangidwa kuti boma lifotokoze bwino chifukwa chimene mafuta […]
The post Boma lati likubweza ngongole ya US$800 miliyoni yomwe inatenga DPP appeared first on Malawi24.