Bungwe la a katswiri pa nkhani za zachuma la Financial Market Dealers Association (FIMDA), lalangiza boma la Malawi kuti liganize zosiya kupeleka ndalama mu ndondomeko ya mtukula pa khomo ndi kuyamba kupeleka zinthu ngati chimanga, ufa ndi zina. Izi ndi malingana ndi mtsogoleri wa bungwe la FIMDA a Leslie Fatch omwe amayankhula Lachisanu munzinda wa […]
The post Boma lalangizidwa kusiya kupeleka ndalama mu ndondomeko ya mtukula pakhomo appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
