Boma lakweza ngongole yomwe ophunzira sukulu za Ukachenjede amalandira

Nduna yoona za chuma mdziko muno a Simplex Chithyola Banda walengeza za kukwera kwa ngongole yomwe ophunzira a msukulu za ukachenjede amalandira kuchoka pa K350, 000 pachaka kufika pa K560,000. A Chithyola Banda anena izi lero masana m’nyumba ya malamulo poyankhapo kutsatira madando omwe zipani zotsutsa boma komanso makomiti ena adapereka m’nyumbayi pankhani yofuna kukweza […]

The post Boma lakweza ngongole yomwe ophunzira sukulu za Ukachenjede amalandira appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください