Boma lakhazikitsa mtengo watsopano wa chiphaso choyendera

Boma la Malawi kudzera ku nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka mdziko muno ya DICS, tsopano yakhazikitsa mtengo wa K50,000 ngati mtengo wa tsopano wa chiphaso choyendera cha anthu wamba. Nkhaniyi ikudza pomwe nthambi ya DICS Lachitatu sabata yatha inalengeza kudzera mu kalata yomwe inatulutsa yosainidwa ndi mkulu wa nthambiyi a Brigadier Charles Kalumo, […]

The post Boma lakhazikitsa mtengo watsopano wa chiphaso choyendera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください