Boma lalengeza kuti lathetsa mlandu wa anthu atatu omwe anawanjata kamba kosokoneza galimoto zapa m’dipiti wa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pomwe ankakakwera ndege ku Chileka mu mzinda wa Blantyre. Omwe amazengedwa mulanduwu ndi a Pearson Chimimba azaka 48, a Lucy Namba azaka 48 komanso a Hector Ndawala azaka 38 zakubadwa. Anthu atatuwa […]
The post Boma lachotsa mlandu wa anthu osokoneza m’dipiti wamtsogoleri appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 