Unduna wa za ma maphunziro mogwirizana ndi bungwe la Malawi Communication Regulatory Authority (MACRA) wakhazikitsa gawo lachiwiri la maphunziro kwa anthu amene amaphunzitsa chiyankhulo cha manja kwa anthu amene ali ndi ulumali . Maphunzirowa amene akuchitikira Ku Mponela mu boma la Dowa athandizira kupitsa pa tsogolo kaphunzilidwe ka chiyankhulo cha manja kwa anthu amene ali […]
The post Boma lachititsa maphunziro kwa aphunzitsi a ophunzira amene ali ndi ulumali appeared first on Malawi 24.