Mkulu wa Mwanza Social Welfare, a Mary Msidwa, ati boma la Mwanza lakwanitsa kuthetsa maukwati a ana achichepere okwana 118 mu chaka cha 2023. A Msindwa anena izizi lero pamene anali ndi zokambilana ndi khosolo la boma la Zomba komaso bungwe la Save the Children pa mutu oti “Kuthetsa maukwati a ana achichepere”. Iwo ati […]
The post Boma la Mwanza lakwanitsa kuthesa ma ukwati a ana okwana 118 appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 