Boma la a Chakwera lakwiyitsa America pa zakatangale

Dziko la United states of America lati ndilokhumudwa kuti boma la Tonse motsogozedwa ndi a Lazarus Chakwera silikuonetsa chidwi chofuna kuthana ndi katangale mdziko muno. Izi ndimalingana ndi chikalata chomwe ofesi ya Kazembe wa dziko la America kuno ku Malawi latulutsa lero potsatira ganizo la boma lofuna kuchotsa chiletso cha bwalo la milandu chomwe chabwenzeretsa […]

The post Boma la a Chakwera lakwiyitsa America pa zakatangale appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください