Phungu wa nyumba ya malamulo wa dera lapakati mu mzinda wa Lilongwe Alfred Jiya wapempha boma kuti lichite machawi popeleka zipangizo za ulimi zotsika mitengo kwa anthu okhala m’madera amatawuni ponena kuti nawo ali ndi minda komanso amafuna kukhala ndi chakudya chokwanila. Iye walakhula izi m’nyumba ya malamulo lachiwiri sabata ino pomwe anafunsa funso nduna […]
The post Boma alipempha kuti lichite changu popeleka zipangizo za ulimi appeared first on Malawi 24.