Anthu m’masamba amchezo ati ndiodabwa kuti kampani yochititsa juga ya Premier Bet yalengeza kuti munthu wina wawina ndalama zokwana K639 miliyoni pomwe malamulo a kampaniyi amati munthu sangawine ndalama zopitilira K500 miliyoni ndipo ena akuti akuona ngati uku nkusatsa malonda chabe. Lolemba pa 15 April, 2024, kampani ya Premier Bet inalengeza kuti mzika ya dziko […]
The post “Bodza ili”: Premier Bet yatutumutsa gulu polengeza kuti munthu wawina K639 miliyoni appeared first on Malawi 24.