Black Nina yemwe ndi oyimba odziwika bwino m’dziko lino, anapita ku malo okwerera ndege ndi mpanda buleki (njinga) wake uku atanyamulirapo chibinyira cha zovala ndicholinga choti akweze njingayo mundege pawulendo wake waku jubeki. Malingana ndi kanema yemwe anthu ena anajambula pozizwa ndi zomwe woyimbayu anapanga, zimaonetsa kuti alonda pamalopo anamubweza nayo njingayi kuti asafike nayo […]
The post Black Nina anatenga njinga yake kuti ‘akweze mundege’ appeared first on Malawi 24.