Mwambo okhadzikitsa Bishop William Mchombo kukhala Bishop wachitatu wa Anglican mu Diocese ya Upper Shire uchitika Loweruka pa 28 May ku St Peters and Paul Cathedral Boma la Mangochi. Wapampambo wa komiti yomwe ikuyendetsa zokonzekera mwambowu a Winasi Boma ati zonse zikuyenda bwino ndipo ali ndichikhulupiliro kuti mwambowu udzakhala wapamwamba. Mtsogoleri wadziko lino a Lazarus […]
The post Bishop William Mchombo amukhazikitsa Loweruka kukhala Bishop wa Anglican Diocese ya Upper Shire appeared first on Malawi 24.