Big Joe ang’alula APM ati ndiwokonda za matsenga, sakhululuka ndipo samva za munthu

Yemwe anali mkulu oyendetsa zinthu [Director of Operations] mu chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) a Joe Nyirongo wayankhula mosapsatira mawu za bwana ake akale a Peter Mutharika kuti ndi munthu wokonda zamatsenga, wosakhululuka ndiponso samva za munthu. A Nyirongo, omwe amatchuka ndi zina loti Big Joe, anena izi pa wailesi ya kanema ya Zodiak […]

The post Big Joe ang’alula APM ati ndiwokonda za matsenga, sakhululuka ndipo samva za munthu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください