Khonsolo ya mzinda wa Blantyre yaopseza kuti igumula nyumba zonse zomwe zikumangidwa m’malo omwe ali pa chiopsezo chokhudzidwa ndi ngozi za chilengedwe monga m’mapili. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe khonsoloyi yatulutsa lachiwiri sabata ino pa 1 August chomwe watikitira ndi mkulu wa khonsoloyi a Dennis Stan Chinseu. BCC yati kumanga m’malo amene ali pachiopsezo […]
The post BCC igumula nyumba zomangidwa malo osayenera appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 