Banki yaikulu ya Reserve yalengeza kuti mabanki akwabwereka ndalama tsopano azipereka chiongola dzanja cha K26 pa K100 iliyonse kuchoka pa K24 pa K100 iliyonse. Bankiyi yalengeza izi kutsatira mkumano omwe inachita pa 31 January mpaka pa 1 February. Mkulu wa RBM a Wilson Banda wati bankiyi inaona kuti katundu akuptilira kukwera ndipo kukweza kwachiongola dzanjaku […]
The post Banki yaikulu yakweza chiongola dzanja appeared first on Malawi 24.