Banki ya dziko lonse yayambanso kuthandiza Malawi

Kwa nthawi yoyamba tsopano kuchokera mchaka cha 2017, banki yayikulu pa dziko lonse ya World Bank yalengeza kuti ipeleka thandizo loti lithandizile mundondomeko yazachuma mdziko lino. Ndipo padakali pano yapereka ndalama zokwana 137 miliyoni dollars zomwe ndi pafupifupi 230 billion kwacha zithandizira ntchito zachuma ndi zina. Izi zadza kudzera mchikalata chomwe bankiyi yatulutsa, iyo yati […]

The post Banki ya dziko lonse yayambanso kuthandiza Malawi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください