Banja la Dan Lu ladzidzimutsa gulu ndi mphatso ya mwana

Kuyelekeza ndi mchaka cha 2017 pomwe oyimba otchuka Dan Lufani anatchuka ndi zithuzi zomwe anaima ndi nkazi wake wake nthawi imeneyo ali  oyembekezera, ulendo uno oyimbayu sanapangeso zakezi ndipo gulu latutumuka pomwe langouzidwa kuti kwabadwa mwana. Dan Lu pamodzi ndi nthiti yake Katerina Nzima lero alandira mphatso ya mwana wa mamuna zomwe anthu ochuluka adabwa […]

The post Banja la Dan Lu ladzidzimutsa gulu ndi mphatso ya mwana appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください