Bambo wina wadzikhweza ku Dowa

Bambo wina ku Dowa  yemwe dzina lake ndi Kelvin Songazaudzu wa zaka 47 zakubadwa wadzimangilira kudenga la nyumba yake kaamba kamavuto a m’banja. Mneneri wa apolisi m’bomali a MacPatson Msadala watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati malemuwa ndi a m’mudzi wa Chimphapa m’dera la mfumu yayikulu Chakhaza ku Dowa komweko. Malingana ndi a Msadala, bamboyu wakhala […]

The post Bambo wina wadzikhweza ku Dowa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください