Bambo wawotcha dzanja la mwana chifukwa cha mondokwa

Bambo wina ku Zomba yemwe dzina lake ndi Ronnex Bandawe wapezeka olakwa pa mlandu oti adawotcha dzanja la mwana wa zaka zisanu ndi chimodzi (6) yemwe ndi mwana wachemwali wabamboyu ati chifukwa adaba chimanga chimodzi. Pakali pano oweruza mlandu Christopher Makumba akuyembekedzeka kudzapereka chigamulo chake pa 18 April mwezi uno. Bungwe la Development Communications Trust […]

The post Bambo wawotcha dzanja la mwana chifukwa cha mondokwa appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください