Bambo wa zaka 32 yemwe dzina lake ndi Dickson Kachikuni ali mu chitokosi cha a polisi ya pa Nkhunga ku Nkhotakota kamba kowaganizira kuti apha mkazi wawo Leah Ngoma wa zaka 21 pomumenya ndi mwala m’mutu pomwe amagona usiku wapa 1 January. Bamboyu akuti amaganizira kuti mkazi wakeyu anali ndi chibwenzi chamseli. Mneneli wapolisi ya […]
The post Bambo wapha mkazi wake pomumenya m’mutu ndi mwala appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 