La fote lakwana! Bambo wina walilime lakuthwa yemwe ndi wa zaka 39 ali m’manja mwa apolisi ku Lilongwe pomuganizira kuti wakhala akufusira amayi pa tsamba la nchezo la fesibuku ndikuwalonjeza kuti awakwatira koma akakumana nawo amawabera katundu kapena ndalama ndikuthawa. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu omwe azindikira […]
The post Bambo wanjatwa kamba kobera amayi omwe amawafunsira pa fesibuku appeared first on Malawi 24.