Bambo wina wa zaka 27, wamwalira pomwe anagwidwa ndi nyesi ya magetsi pomwe amafuna kuba mtchalitchi cha Katolika m’boma la Mangochi. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Monkey Bay a Alice Sichali omwe azindikira malemuwa ngati a Geoffrey Matewere omwe akumana ndi zakudazi Lolemba pa 15 January, 2024. A Sichali ati patsikuli, […]
The post Bambo wafera pa tchalitchi cha Katolika pomwe amafuna kuba appeared first on Malawi 24.