Apolisi m’boma la Mulanje atsimikiza kuti bambo wina wa zaka pafupifupi 70 wamwalira mkati mwa ndime ku malo ena ogonako alendo pomwe anamwa mankhwala a opeleka mphamvu kwa a bambo. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Mulanje a Innocent Moses omwe azindikira zibamboyu ngati a Leman Walama. Moses wati bambo Walama apezeka […]
The post Bambo wafela ku lumu atamwa mankhwala opereka mphamvu kwa bambo appeared first on Malawi 24.