Munthu m’modzi wafa pamene ena 6,145 manja ali ku nkhongo pamene akusowa pokhala kutsatira kusefukira kwa madzi komwe kwa chitika ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota. Malingana ndi lipoti lomwe lachokera ku khosolo ya bomali kudzera ku nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzi, madera omwe akhudzidwa ndi ngoziyi ndi kwa mfumu yaikulu Kanyenda komanso Mphonde. Munthu […]
The post Bambo wafa ndipo anthu 6,145 akusowa mtengo wogwira kamba kakusefukira kwa madzi m’boma la Nkhotakota appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
