Bambo wa zaka 45 wafa m’mudzi wa Maluzi ku Kasungu atakwililika mu mgodi omwe amakumbamo golide. Bamboyu dzina lake ndi Godfrey Chirombo. Malingana ndineneri wa polisi ya Kasungu, Sub-Inspector Jospeh Kachikho, a Chirombo pamodzi ndi mwana wawo analowera ku mtsinje wa Chithimbiri womwe uli m’deralo kuti akafukule mwala golide Mwana wawoyo anawasiya kaye a Chirombo […]
The post Bambo wafa mgodi wa golide utadilizika ku Kasungu appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 