Bambo wina wa zaka 33, wafa galimoto yomwe amayendetsa momweso munali banja lake itaombedwa ndi sitima ya pa mtunda pa malo owolokera ku Machinga komwe anapita ku tchuthi. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Machinga a Western Kansire omwe azindikira malemuwa ngati a Saul Chitseko. Malingana ndi a Kansire, a Chitseko pamodzi […]
The post Bambo wafa galimoto yake itaombedwa ndi sitima appeared first on Malawi 24.