Bambo wa zaka 38 mu mzinda wa Lilongwe wadzipha podzimangilira ku denga la nyumba yake atazindikira kuti abale ake adziwa kuti iye anaba nkhuku ya m’bale wake. Watsimikiza za nkhaniyi ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani pa polisi ya munzinda wa Lilongwe mayi Khumbo Sanyiwa omwe azindikira malemuwa ngati a Davison Sitima. Sanyiwa wati bambo Sitima […]
The post Bambo wadzipha ataba nkhuku appeared first on Malawi 24.